2 Samueli 2:5 BL92

5 Pamenepo Davide anatumiza mithenga kwa anthu a ku Jabezi Gileadi, nanena nao, Mudalitsike ndi Yehova inu, popeza munacitira cokoma ici mbuye wanu Sauli, ndi kumuika.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:5 nkhani