2 Samueli 2:6 BL92

6 Ndipo tsopano Yehova acitire inu cokoma ndi coonadi; inenso ndidzakubwezerani cokoma ici, popeza munacita cinthuci.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:6 nkhani