2 Samueli 20:1 BL92

1 Ndipo kudangotero kuti pamenepo panali munthu woipa, dzina lace ndiye Seba mwana wa Bikri Mbenjamini; naliza iye lipenga, nati, Ife tiribe gawo mwa Davide, tiribenso colowa mwa mwana wa Jese; munthu yense apite ku mahema ace, Israyeli inu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20

Onani 2 Samueli 20:1 nkhani