2 Comweco anthu onse a Israyeli analeka kutsata Davide, natsata Seba mwana wa Bikri; koma anthu a Yuda anaphatikizana ndi mfumu yao, kuyambira ku Yordano kufikira ku Yerusalemu.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20
Onani 2 Samueli 20:2 nkhani