2 Samueli 20:10 BL92

10 Koma Amasa sanasamalira lupanga liri m'dzanja la Yoabu; comweco iye anamgwaza nalo m'mimba; nakhuthula matumbo ace pansi, osamgwazanso; nafa iye, Ndipo Yoabu ndi Abisai mbale wace analondola Seba mwana wa Bikri.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20

Onani 2 Samueli 20:10 nkhani