2 Samueli 20:9 BL92

9 Ndipo Yoabu ananena ndi Amasa, Uli bwino mbale wanga? Ndipo Yoabu anagwira ndebvu za Amasa ndi dzanja lace lamanja kuti ampsompsone.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20

Onani 2 Samueli 20:9 nkhani