2 Samueli 20:8 BL92

8 Pamene anafika iwo pa mwala waukuru uli ku Gibeoni, Amasa anadza kukomana nao. Ndipo Yoabu atabvala mwinjiro wace, anadzimangirira lamba lolongamo lupanga m'cimace m'cuuno mwace; ndipo m'kuyenda kwace lidasololoka.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20

Onani 2 Samueli 20:8 nkhani