7 Ndipo anaturuka namtsata anthu a Yoabu, ndi Akereti ndi Apeleti, ndi anthu onseamphamvu; naturuka m'Yerusalemu kukalondola Seba mwana wa Bikri.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20
Onani 2 Samueli 20:7 nkhani