2 Samueli 21:1 BL92

1 Ndipo m'masiku a Davide munali odala, zaka zitatu; ndipo Davide anafunsira kwa Yehova. Ndipo Yehova anati, Ndico cifukwa ca Sauli ndi nyumba yace yamwazi, popeza iye anawapha Agibeoni.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21

Onani 2 Samueli 21:1 nkhani