2 Samueli 21:2 BL92

2 Ndipo mfumu inaitana Agibeoni, ninena nao (koma Agibeoni sanali a ana a Israyeli, koma a Aamori otsala; ndipo ana a Israyeli anawalumbirira kwa iwo, koma Sauli anafuna kuwapha mwa cangu cace ca kwa ana a Israyeli ndi a Yuda).

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21

Onani 2 Samueli 21:2 nkhani