2 Samueli 21:10 BL92

10 Ndipo Rizipa mwana wamkazi wa Aya anatenga ciguduli, nadziyalira ici pathanthwe, kuyambira pakukolola kufikira madzi ocokera kumwamba adawagwera; ndipo sadalola mbalame za m'mlengalenga kutera pa iwo usana, kapena zirombo za kuthengo usiku.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21

Onani 2 Samueli 21:10 nkhani