16 Ndipo Isibenobi, ndiye wa ana a Rafa, amene kulemera kwa mkondo wace kunali masekeli mazana atatu a mkuwa, iyeyo anabvala lupanga latsopano, nati aphe Davide.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21
Onani 2 Samueli 21:16 nkhani