2 Samueli 21:17 BL92

17 Koma Abisai mwana wa Zeruya anamthandiza namkantha Mfliistiyo, namupha. Pomwepo anthu a Davide anamlumbirira iye nati, Inu simudzaturuka nafenso kunkhondo, kuti mungazime nyali ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21

Onani 2 Samueli 21:17 nkhani