2 Samueli 22:25 BL92

25 Cifukwa cace Yehova anandibwezera monga mwa colungama canga;Monga mwa kuyera kwanga pamaso pace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 22

Onani 2 Samueli 22:25 nkhani