17 Nati, Ndisacite ici ndi pang'ono ponse, Yehova; ndimwe kodi mwazi wa anthu awa ana pitawa ndi kutaya moyo wao? Cifukwa cace iye anakana kumwa. Izi anazicita ngwazi zitatuzi.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 23
Onani 2 Samueli 23:17 nkhani