18 Ndipo Abisai, mbale wa Yoabu, mwana wa Zeruya, anali wamkuru wa atatuwa. Iye natukula mkondo wace pa anthu mazana atatu nawapha, natenga dzina iye mwa atatuwa.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 23
Onani 2 Samueli 23:18 nkhani