2 Samueli 24:1 BL92

1 Ndipo mkwiyo wa Yehova unayakanso pa Israyeli, nafulumiza Davide pa iwo, nati, Muka, nuwerenge Israyeli ndi Yuda.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:1 nkhani