2 Samueli 24:2 BL92

2 Ndipo mfumu inanena ndi Yoabu kazembe wa khamu, amene anali naye, Kayendere tsopano mafuko onse a Israyeli, kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba, nuwerenge anthuwo, kuti ndidziwe kucuruka kwao kwa anthu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:2 nkhani