2 Samueli 24:14 BL92

14 Ndipo Davide ananena ndi Gadi, Ndipsinjika mtima kwambiri, tigwe m'dzanja la Yehova; pakuti zifundo zace nzazikuru; koma tisagwe m'dzanja la munthu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:14 nkhani