2 Samueli 24:15 BL92

15 Comweco Yehova anatumiza mliri pa Israyeli kuyambira m'mawa kufikira nthawi yoikika; ndipo anafapo anthu zikwi makumi asanu ndi awiri kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:15 nkhani