2 Samueli 24:21 BL92

21 Arauna nati, Mbuye wanga mfumu, mwadzeranji kwa mnyamata wanu? Ndipo Davide anati, Kugula dwale lako gi, kuti ndimangirepo Yehova guwa lansembe, kuti mliriwo ulekeke kwa anthu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:21 nkhani