2 Samueli 24:22 BL92

22 Arauna nati kwa Davide, Mbuye wanga mfumu atenge napereke nsembe comkomera; sizi ng'ombe za nsembe yopsereza, ndi zipangizo ndi zomangira ng'ombe zikhale nkhuni;

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:22 nkhani