2 Samueli 24:24 BL92

24 Koma mfumu inati kwa Arauna, lai; koma ndidzaligula kwa iwe pa mtengo wace, pakuti sindidzapereka kwa Yehova Mulungu wanga nsembe zopsereza zopanda mtengo wace. Momwemo Davide anagula dwalelo ndi ng'ombezo naperekapo masekeli makumi asanu a siliva.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:24 nkhani