2 Samueli 24:25 BL92

25 Ndipo Davide anamangirapo Yehova guwa la nsembe, napereka nsembe zopsereza, ndi nsembe zoyamika. Momwemo Yehova anapembedzeka cifukwa ca dziko, ndi mliri wa pa Israyeli unalekeka.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:25 nkhani