2 Samueli 24:4 BL92

4 Koma mau a mfumu anapambana Yoabu ndi atsogoleri a khamulo. Ndipo Yoabu ndi atsogoleri a khamulo anaturuka pamaso pa mfumu kuti akawerenge anthu a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:4 nkhani