2 Samueli 3:22 BL92

22 Ndipo taonani, anyamata a Davide ndi Yoabu anabwera kucokera ku nkhondo yobvumbulukira, nakhala nazo zofunkha zambiri. Koma Abineri sanali ku Hebroni kwa Davide, cifukwa adalawirana naye ndipo adamuka mumtendere.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3

Onani 2 Samueli 3:22 nkhani