2 Samueli 3:23 BL92

23 Tsono pofika Yoabu ndi khamu lonse anali nalo, ena anamfotokozera Yoabu nati, Abineri mwana wa Neri anabwera kwa mfumu, amene analawirana naye, namuka iye mumtendereo

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3

Onani 2 Samueli 3:23 nkhani