12 Ndipo Davide analamulira anyamata ace, iwo nawapha, nawapacika m'mbali mwa thamanda ku Hebroni atawadula manja ndi mapazi ao. Koma mutu wa Isiboseti anautenga nauika m'manda a Abineri ku Hebroni.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 4
Onani 2 Samueli 4:12 nkhani