2 Samueli 5:1 BL92

1 Pomwepo mafuko onse a Israyeli anabwera kwa Davide ku Hebroni, nalankhula nati, Taonani, ife ndife pfupa lanu ndi mnofu wanu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 5

Onani 2 Samueli 5:1 nkhani