2 Samueli 4:5 BL92

5 Ndipo Rekabu ndi Baana ana a Rimoni wa ku Beeroti, anamuka, nafika ku nyumba ya Isiboseti potentha dzuwa popumula iye usana.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 4

Onani 2 Samueli 4:5 nkhani