2 Samueli 6:16 BL92

16 Ndipo kunali pamene likasa la Yehova tinafika m'mudzi wa Davide, Mikala mwana wamkazi wa Sauli, analikupenya pazenera, naona mfumu Davide alikubvina ndi kusewera pamaso pa Yehova, nampeputsa mumtima mwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 6

Onani 2 Samueli 6:16 nkhani