2 Samueli 6:15 BL92

15 Comweco Davide ndi a nyumba yonse ya Israyeli anakwera nalo likasa la Yehova, ndi cimwemwe ndi kulira kwa malipenga,

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 6

Onani 2 Samueli 6:15 nkhani