2 Samueli 6:5 BL92

5 Ndipo Davide ndi a nyumba yonse ya Israyeli anasewera pamaso pa Yehova, ndi zoyimbira za mitundu mitundu za mlombwa, ndi azeze, ndi zisakasa ndi malingaka, ndi masece, ndi nsanje.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 6

Onani 2 Samueli 6:5 nkhani