2 Samueli 6:6 BL92

6 Ndipo pofika iwo ku dwale la Nakoni, Uza anatambasula dzanja lace, nacirikiza likasa la Mulungu; cifukwa ng'ombe zikadapulumuka.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 6

Onani 2 Samueli 6:6 nkhani