2 Samueli 6:7 BL92

7 Pomwepo mkwiyo wa Yehova udayaka pa Uza, ndipo Mulungu anamkantha pomwepo, cifukwa ca kusalingiriraku; nafa iye pomwepo pa likasa la Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 6

Onani 2 Samueli 6:7 nkhani