16 Ndipo nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikikadi ku nthawi zonse pamaso pako; mpando wacifumu wako udzakhazikika ku nthawi zonse.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7
Onani 2 Samueli 7:16 nkhani