17 Monga mwa mau onse awa ndi monga mwa masomphenya onse awa, momwemo Natani analankhula ndi Davide.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7
Onani 2 Samueli 7:17 nkhani