18 Pomwepo Davide mfumu analowa, nakhalapansi pamaso pa Yehova; nati, Ine ndine yani, Yehova Mulungu, ndi banja langa ndi ciani kuti munandifikitsa pano?
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7
Onani 2 Samueli 7:18 nkhani