2 Samueli 8:5 BL92

5 Ndipo pakufika Aaramu a ku Damasiko kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya ku Zoba, Davide anakanthako Aaramu zikwi makumi awiri mphambu ziwiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 8

Onani 2 Samueli 8:5 nkhani