6 Pamenepo Davide anaika maboma m'Aramu wa Damasiko, Ndipo Aaramu anasanduka anthu a Davide, nabwera nayo mitulo. Ndipo Yehova anamsunga Davide kuli konse anamukako.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 8
Onani 2 Samueli 8:6 nkhani