2 Samueli 9:2 BL92

2 Ndipo panali mnyamata wa m'nyumba ya Sauli dzina lace Ziba; ndipo anamuitana iye afike kwa Davide; ndi mfumuyo inanena naye, Iwe ndiwe Ziba kodi? Nati iye, Ndine mnyamata wanu ame.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 9

Onani 2 Samueli 9:2 nkhani