2 Samueli 9:3 BL92

3 Ndipo mfumu inati, Kodi atsalanso wina wa nyumba ya Sauli kuti ndimuonetsere cifundo ca Mulungu? Ziba nanena ndi mfumu, Aliponso mwana wa Jonatani wopunduka mapazi ace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 9

Onani 2 Samueli 9:3 nkhani