2 Samueli 9:7 BL92

7 Ndipo Davide ananena naye, Usaopa, pakuti zoonadi ndidzakucitira kukoma mtima cifukwa ca Jonatani atate wako; ndi minda yonse ya Sauli ndidzakubwezera, ndipo udzadya pa gome langa cikhalire.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 9

Onani 2 Samueli 9:7 nkhani