1 CIBVUMBULUTSO ca Yesu Kristu, cimene Mulungu anambvumbulutsira acionetsere akapolo ace, ndico ca izi ziyenera kucitika posacedwa: ndipo potuma mwa mngelo wace anazindikiritsa izi kwa kapolo wace Yohane;
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 1
Onani Cibvumbulutso 1:1 nkhani