Cibvumbulutso 1:13 BL92

13 ndipo pakati pa zoikapo nyalizo wina wonga Mwana wa munthu atabvala cobvala cofikira ku mapazi ace, atamangira lamba lagolidi pacifuwa.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 1

Onani Cibvumbulutso 1:13 nkhani