Cibvumbulutso 1:17 BL92

17 Ndipo pamene ndinamuona iye, ndinagwa pa mapazi ace ngati wakufa; ndipo anaika dzanja lace lamanja pa ine, nati, Usaope, ine ndine woyamba ndi wotsiriza,

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 1

Onani Cibvumbulutso 1:17 nkhani