9 Ine Yohane, mbale wanu ndi woyanjana nanu m'cisautso ndi ufumu ndi cipiriro zokhala m'Yesu, ndinakhala pa cisumbu cochedwa Patmo, cifukwa ca mao a Mulungu ndi umboni wa Yesu.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 1
Onani Cibvumbulutso 1:9 nkhani