Cibvumbulutso 11:2 BL92

2 Ndipo bwalo la kunja kwa Kacisi ulisiye padera, osaliyesa; pakuti adapatsa ilo kwa amitundu; ndipo mzinda wopatulika adzaupondereza miyezi makumi anai mphambu iwiri.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 11

Onani Cibvumbulutso 11:2 nkhani