Cibvumbulutso 12:14 BL92

14 Ndipo anapatsa mkazi mapiko awiri a ciombankhanga cacikuru, kuti akaulukire kucipululu, ku mbuto yace, kumene adyetsedwako nthawi, ndi zinthawi, ndi nusu la nthawi, osapenya nkhope ya njoka.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 12

Onani Cibvumbulutso 12:14 nkhani