Cibvumbulutso 12:17 BL92

17 Ndipo cinjoka cinakwiya ndi mkazi, nicinacoka kunka kucita nkhondondi otsala ambeu yace, amene asunga malamulo a Mulungu, nakhala nao umboni wa Yesu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 12

Onani Cibvumbulutso 12:17 nkhani